Arabic with tafsir
Listen to Surah Al-Falaq (1299 reciters)
بِسۡمِ ٱللَّهِ ٱلرَّحۡمَٰنِ ٱلرَّحِيمِ
قُلۡ أَعُوذُ بِرَبِّ ٱلۡفَلَقِ ١Nena: “Ine ndifuna kuthawira kwa Ambuye wa M’mbandakucha مِن شَرِّ مَا خَلَقَ ٢Kuchokera ku zinthu zonyansa zimene walenga وَمِن شَرِّ غَاسِقٍ إِذَا وَقَبَ ٣Ndi kuchokera ku zonyansa za nthawi ya usiku pamene mdima ufika وَمِن شَرِّ ٱلنَّفَّٰثَٰتِ فِي ٱلۡعُقَدِ ٤Ndi kuchokera ku zonyansa za anthu a matsenga pamene auzila pfundo وَمِن شَرِّ حَاسِدٍ إِذَا حَسَدَ ٥“Ndi ku zonyansa za munthu wa dumbo pamene achita nsanje.”
Translation: Al Haji Yusuf Muhammad Kanyamula.