Millat al-Islam

Chapter 110 · 3 verses · Al Haji Yusuf Muhammad Kanyamula

Surah An-Nasr in Chichewa

Arabic with tafsir Listen to Surah An-Nasr (1288 reciters)
Medinanسورة النصر3 verses

بِسۡمِ ٱللَّهِ ٱلرَّحۡمَٰنِ ٱلرَّحِيمِ

إِذَا جَآءَ نَصۡرُ ٱللَّهِ وَٱلۡفَتۡحُ ١Pamene chithandizo cha Mulungu chidza ndi kupambana وَرَأَيۡتَ ٱلنَّاسَ يَدۡخُلُونَ فِي دِينِ ٱللَّهِ أَفۡوَاجًا ٢Ndipo uona anthu akulowa m’chipembedzo cha Mulungu mu unyinji wawo فَسَبِّحۡ بِحَمۡدِ رَبِّكَ وَٱسۡتَغۡفِرۡهُۚ إِنَّهُۥ كَانَ تَوَّابَۢا ٣Motero lemekeza Ambuye wako ndipo upemphe chikhululukiro chake. Ndithudi Iye amavomera kulapa ndipo ndi wokhululukira

Translation: Al Haji Yusuf Muhammad Kanyamula.