Millat al-Islam

Chapter 91 · 15 verses · Al Haji Yusuf Muhammad Kanyamula

Surah Ash-Shams in Chichewa

Arabic with tafsir Listen to Surah Ash-Shams (1346 reciters)
Meccanسورة الشمس15 verses

بِسۡمِ ٱللَّهِ ٱلرَّحۡمَٰنِ ٱلرَّحِيمِ

وَٱلشَّمۡسِ وَضُحَىٰهَا ١Pali dzuwa ndi kuwala kwake وَٱلۡقَمَرِ إِذَا تَلَىٰهَا ٢Ndi pali mwezi umene umatuluka dzuwa litalowa وَٱلنَّهَارِ إِذَا جَلَّىٰهَا ٣Ndi masana pamene kumayera وَٱلَّيۡلِ إِذَا يَغۡشَىٰهَا ٤Ndi pali usiku umene umabisa وَٱلسَّمَآءِ وَمَا بَنَىٰهَا ٥Ndi pali Kumwamba ndi Iye amene adakulenga وَٱلۡأَرۡضِ وَمَا طَحَىٰهَا ٦Ndi pali dziko lapansi ndi Iye amene analitambasula وَنَفۡسٍ وَمَا سَوَّىٰهَا ٧Ndi pali mzimu ndi Iye amene adaulenga فَأَلۡهَمَهَا فُجُورَهَا وَتَقۡوَىٰهَا ٨Ndi kumupatsa iye nzeru zodziwa choipa ndi chabwino قَدۡ أَفۡلَحَ مَن زَكَّىٰهَا ٩Ndithudi wopambana ndi amene amadziyeretsa وَقَدۡ خَابَ مَن دَسَّىٰهَا ١٠Ndipo wolephera ndiye amene wadzidetsa كَذَّبَتۡ ثَمُودُ بِطَغۡوَىٰهَآ ١١Anthu a Thamoud adakana Mtumwi wawo poukiramoyerekedwa إِذِ ٱنۢبَعَثَ أَشۡقَىٰهَا ١٢Pamenemunthuolakwakwambiri adayambitsa chipolowe فَقَالَ لَهُمۡ رَسُولُ ٱللَّهِ نَاقَةَ ٱللَّهِ وَسُقۡيَٰهَا ١٣Ndipo Mthenga wa Mulungu anati kwa iwo: “Samalirani ngamira ya ikazi ya Mulungu ndi tsiku lake lomwa madzi!” فَكَذَّبُوهُ فَعَقَرُوهَا فَدَمۡدَمَ عَلَيۡهِمۡ رَبُّهُم بِذَنۢبِهِمۡ فَسَوَّىٰهَا ١٤Iwo sadakhulupirire ayi ndipo ngamirayo adaipha. Motero Ambuye wawo adawaononga chifukwa cha machimo awo ndipo adafafaniza onse mosasankha وَلَا يَخَافُ عُقۡبَٰهَا ١٥Iye sadaope chotsatira chake

Translation: Al Haji Yusuf Muhammad Kanyamula.