Millat al-Islam

Chapter 108 · 3 verses · Khaled Ibrahim Betala

Surah Al-Kawthar in Chichewa

Arabic with tafsir Listen to Surah Al-Kawthar (810 reciters)
Meccanسورة الكوثر3 verses

بِسۡمِ ٱللَّهِ ٱلرَّحۡمَٰنِ ٱلرَّحِيمِ

إِنَّآ أَعۡطَيۡنَٰكَ ٱلۡكَوۡثَرَ ١“Ndithu takupatsa zabwino zambiri (zina mwa izo ndi mtsinje wotchedwa Kauthar) فَصَلِّ لِرَبِّكَ وَٱنۡحَرۡ ٢“(Pakuti ndakupatsa zimenezo), pitiriza kupembedza Mbuye wako (moyera mtima) ndipo ipha nsembe yako (chifukwa chakuthokoza Allah pa zimene wakupatsa, monga ulemelero ndikukusankhira zabwino zambiri) إِنَّ شَانِئَكَ هُوَ ٱلۡأَبۡتَرُ ٣“Ndithu mdani wako ndiye ali wopanda mwawi

Translation: Khaled Ibrahim Betala.