بِسۡمِ ٱللَّهِ ٱلرَّحۡمَٰنِ ٱلرَّحِيمِ
هَلۡ أَتَىٰكَ حَدِيثُ ٱلۡغَٰشِيَةِ ١Kodi wamva za chinthu chachikulu chimene chili nkudza وُجُوهٌ يَوۡمَئِذٍ خَٰشِعَةٌ ٢Nkhope zina, patsiku limeneli, zidzachititsidwa manyazi عَامِلَةٌ نَّاصِبَةٌ ٣Pogwira ntchito zotopetsa تَصۡلَىٰ نَارًا حَامِيَةً ٤Iwo adzalowa kumoto woyaka تُسۡقَىٰ مِنۡ عَيۡنٍ ءَانِيَةٍ ٥Iwo adzapatsidwa madzi oti amwe kuchokera kuchitsime cha moto لَّيۡسَ لَهُمۡ طَعَامٌ إِلَّا مِن ضَرِيعٍ ٦Sadzakhala ndi chakudya china koma chiphe cha mtengo waminga لَّا يُسۡمِنُ وَلَا يُغۡنِي مِن جُوعٍ ٧Chimene sichidzawapatsa thanzi kapena kuthetsa njala وُجُوهٌ يَوۡمَئِذٍ نَّاعِمَةٌ ٨Nkhope zina, pa tsikuli, zidzakhala zosangalala لِّسَعۡيِهَا رَاضِيَةٌ ٩Adzakondwa chifukwa cha ntchito zawo فِي جَنَّةٍ عَالِيَةٍ ١٠Atakhala m’minda ya pamwamba لَّا تَسۡمَعُ فِيهَا لَٰغِيَةً ١١Kumene iwo sadzamva zoononga kapena za bodza فِيهَا عَيۡنٌ جَارِيَةٌ ١٢Mudzakhala kasupe wa madzi oyenda فِيهَا سُرُرٌ مَّرۡفُوعَةٌ ١٣Ndi mipando yonyamuka ya wofowofo وَأَكۡوَابٌ مَّوۡضُوعَةٌ ١٤Ndi zikho zomwera zitaikidwa pambali pake وَنَمَارِقُ مَصۡفُوفَةٌ ١٥Ndi makushoni yoikidwa m’mizere وَزَرَابِيُّ مَبۡثُوثَةٌ ١٦Ndi mikeka yoyalidwa bwino pansi pake أَفَلَا يَنظُرُونَ إِلَى ٱلۡإِبِلِ كَيۡفَ خُلِقَتۡ ١٧Kodi iwo saona mmene ngamira zidalengedwera وَإِلَى ٱلسَّمَآءِ كَيۡفَ رُفِعَتۡ ١٨Ndi Kumwamba mmene kudakwezedwera وَإِلَى ٱلۡجِبَالِ كَيۡفَ نُصِبَتۡ ١٩Ndi mapiri mmene adalengedwera mokhazikika وَإِلَى ٱلۡأَرۡضِ كَيۡفَ سُطِحَتۡ ٢٠Ndi dziko mmene adalitambasulira فَذَكِّرۡ إِنَّمَآ أَنتَ مُذَكِّرٌ ٢١Motero akumbutse, chifukwa udindo wako ndi wowakumbutsa لَّسۡتَ عَلَيۡهِم بِمُصَيۡطِرٍ ٢٢Iwe sindiwe munthu wowakakamiza ayi إِلَّا مَن تَوَلَّىٰ وَكَفَرَ ٢٣Kupatula iye Al Fajr 651 amene abwerera m’mbuyo ndi kuyamba kusakhulupirira فَيُعَذِّبُهُ ٱللَّهُ ٱلۡعَذَابَ ٱلۡأَكۡبَرَ ٢٤Motero Mulungu adzamulanga chilango chachikulu إِنَّ إِلَيۡنَآ إِيَابَهُمۡ ٢٥Ndithudi onse adzabwerera kwa Ife ثُمَّ إِنَّ عَلَيۡنَا حِسَابَهُم ٢٦Ndipo, ndithudi, chiwerengero cha zochita zawo chidzakhala kwa Ife