ملة الإسلام

السورة 109 · 6 آية · Khaled Ibrahim Betala

سورة الكافرون باللغة الشيشيوا

السورة بالعربية مع التفسير استمع إلى سورة الكافرون (786 قارئاً)
مكيةسورة الكافرون٦ آية

بِسۡمِ ٱللَّهِ ٱلرَّحۡمَٰنِ ٱلرَّحِيمِ

قُلۡ يَٰٓأَيُّهَا ٱلۡكَٰفِرُونَ ١“Nena (iwe Mtumiki) (s.a.w): E inu anthu osakhulupirira لَآ أَعۡبُدُ مَا تَعۡبُدُونَ ٢“Sindipembedza chimene inu mukuchipembedza (kusiya Allah) وَلَآ أَنتُمۡ عَٰبِدُونَ مَآ أَعۡبُدُ ٣“Inunso simumpembedza amene ine ndikumpembedza (yemwe ndi Allah) وَلَآ أَنَا۠ عَابِدٌ مَّا عَبَدتُّمۡ ٤“Ndiponso ine sindidzapembedza chimene inu mwakhala mukuchipembedza (chifukwa inu ndinu ophatikiza Allah ndi zinthu zina) وَلَآ أَنتُمۡ عَٰبِدُونَ مَآ أَعۡبُدُ ٥“Ndipo inu simudzampembedza amene ine ndikumpembedza (yemwe ndi Allah) لَكُمۡ دِينُكُمۡ وَلِيَ دِينِ ٦“Inu muli ndi chipembedzo chanu (chimene mukuchikhulupirira), inenso ndili ndi chipembedzo changa (chimene Allah wandisankhira)

الترجمة: Khaled Ibrahim Betala.