السورة بالعربية مع التفسير
استمع إلى سورة الناس (1,329 قارئاً)
بِسۡمِ ٱللَّهِ ٱلرَّحۡمَٰنِ ٱلرَّحِيمِ
قُلۡ أَعُوذُ بِرَبِّ ٱلنَّاسِ ١“Nena: “Ndikudzitchinjiriza ndi Mbuye (Mleri) wa anthu (Yemwe akulinganiza zinthu zawo) مَلِكِ ٱلنَّاسِ ٢“Mfumu ya anthu ( Imene iri ndi mphamvu yochita chirichonse pa iwo) إِلَٰهِ ٱلنَّاسِ ٣“Wopembedzedwa wa anthu مِن شَرِّ ٱلۡوَسۡوَاسِ ٱلۡخَنَّاسِ ٤“Kuzoipa za mnong’onezi (yemwe amathira unong’onezi wake m’mitimaya anthu) yemwenso amabisala (posiya unong’onezi wake ngati mwini mtimawo atankumbukira Allah) ٱلَّذِي يُوَسۡوِسُ فِي صُدُورِ ٱلنَّاسِ ٥“Yemwe amanong’oneza mzifuwa za anthu مِنَ ٱلۡجِنَّةِ وَٱلنَّاسِ ٦“Wochokera m’ziwanda ndi mwa anthu.”
الترجمة: Khaled Ibrahim Betala.