ملة الإسلام

السورة 94 · 8 آية · Khaled Ibrahim Betala

سورة الشرح باللغة الشيشيوا

السورة بالعربية مع التفسير استمع إلى سورة الشرح (1,296 قارئاً)
مكيةسورة الشرح٨ آية

بِسۡمِ ٱللَّهِ ٱلرَّحۡمَٰنِ ٱلرَّحِيمِ

أَلَمۡ نَشۡرَحۡ لَكَ صَدۡرَكَ ١“Kodi sitidachiphanule chifuwa chako (pokupatsa chiongoko ndi chikhulupiliro ndi nzeru zambiri) وَوَضَعۡنَا عَنكَ وِزۡرَكَ ٢“Ndipo takuchotsera mtolo wako (pa ntchito yolalikira pokuthandiza ndi kukufewetsera zinthu zako) ٱلَّذِيٓ أَنقَضَ ظَهۡرَكَ ٣“Mtolo umene udalemetsa msana wako وَرَفَعۡنَا لَكَ ذِكۡرَكَ ٤“Ndipo takukweza kutchulidwa kwako فَإِنَّ مَعَ ٱلۡعُسۡرِ يُسۡرًا ٥“Ndipo ndithu pali chovuta palinso zabwino (Zambiri) إِنَّ مَعَ ٱلۡعُسۡرِ يُسۡرًا ٦“Ndithu pali chovuta palinso zabwino (zambiri) فَإِذَا فَرَغۡتَ فَٱنصَبۡ ٧“Basi, ukamaliza ntchito (yolalikira ndi Jihâd) limbikira kupemphera وَإِلَىٰ رَبِّكَ فَٱرۡغَب ٨“Ndipo khala wolakalaka (zabwino zomwe zili) kwa Mbuye wako

الترجمة: Khaled Ibrahim Betala.