بِسۡمِ ٱللَّهِ ٱلرَّحۡمَٰنِ ٱلرَّحِيمِ
عَبَسَ وَتَوَلَّىٰٓ ١Iye anachita matsinya ndi kuyang’ana kumbali أَن جَآءَهُ ٱلۡأَعۡمَىٰ ٢Chifukwa munthu wakhungu anadza kwa iye وَمَا يُدۡرِيكَ لَعَلَّهُۥ يَزَّكَّىٰٓ ٣Ndipo iwe ungadziwe bwanji kuti mwina angadziyeretse أَوۡ يَذَّكَّرُ فَتَنفَعَهُ ٱلذِّكۡرَىٰٓ ٤Kapena iye adzalandira chenjezo ndipo chenjezo likanamupindulira kanthu kena أَمَّا مَنِ ٱسۡتَغۡنَىٰ ٥Koma iye amene amadziyesa kuti sasowa kanthu فَأَنتَ لَهُۥ تَصَدَّىٰ ٦Ameneyo ndiye amene uli naye ndi chidwi وَمَا عَلَيۡكَ أَلَّا يَزَّكَّىٰ ٧Kodi uli nazo chiani ngati iye sadziyeretsa وَأَمَّا مَن جَآءَكَ يَسۡعَىٰ ٨Koma kwa iye amene amakuthamangira وَهُوَ يَخۡشَىٰ ٩Ndipo iye amaopa فَأَنتَ عَنۡهُ تَلَهَّىٰ ١٠Iwe siudamulabadire ayi كـَلَّآ إِنَّهَا تَذۡكِرَةٌ ١١Iyayi! Ndithudi chimenechi ndi chikumbutso فَمَن شَآءَ ذَكَرَهُۥ ١٢Muloleni aliyense amene afuna kuti achilabadire فِي صُحُفٍ مُّكَرَّمَةٍ ١٣Ichi chidalembedwa m’Buku la Mulungu lolemekezeka مَّرۡفُوعَةٍ مُّطَهَّرَةِۭ ١٤Loyeretsedwa ndi losungidwa bwino ndi loyera بِأَيۡدِي سَفَرَةٍ ١٥M’manja mwa Alembi كِرَامِۭ بَرَرَةٍ ١٦Wolemekezeka ndipo womvera قُتِلَ ٱلۡإِنسَٰنُ مَآ أَكۡفَرَهُۥ ١٧Atembereredwe munthu! Kodi ndi chiani chili kumuletsa kuthokoza مِنۡ أَيِّ شَيۡءٍ خَلَقَهُۥ ١٨Kodi Iye adamulenga kuchokera ku chiyani مِن نُّطۡفَةٍ خَلَقَهُۥ فَقَدَّرَهُۥ ١٩Kuchokera ku dontho la umuna, Iye adamulenga ndipo adamukonza bwino ثُمَّ ٱلسَّبِيلَ يَسَّرَهُۥ ٢٠Ndipo Iye adamukonzera iye njira yapafupi ثُمَّ أَمَاتَهُۥ فَأَقۡبَرَهُۥ ٢١Ndipo amamupha ndi kumusunga m’manda ثُمَّ إِذَا شَآءَ أَنشَرَهُۥ ٢٢Ndithudi Iye adzamudzutsa monga momwe afunira كـَلَّا لَمَّا يَقۡضِ مَآ أَمَرَهُۥ ٢٣Iyayi, koma munthu sanachite zimene Iye adamulamulira فَلۡيَنظُرِ ٱلۡإِنسَٰنُ إِلَىٰ طَعَامِهِۦٓ ٢٤Mulekeni munthu kuti aganize za chakudya chake أَنَّا صَبَبۡنَا ٱلۡمَآءَ صَبًّا ٢٥Kuti Ife timagwetsa mvula yambiri ثُمَّ شَقَقۡنَا ٱلۡأَرۡضَ شَقًّا ٢٦Ndipo timaphwanya nthaka فَأَنۢبَتۡنَا فِيهَا حَبًّا ٢٧Ndipo Ife Al-Takwir 641 timameretsa njere وَعِنَبًا وَقَضۡبًا ٢٨Mphesa ndi Msipu وَزَيۡتُونًا وَنَخۡلًا ٢٩Mitengo ya mafuta, ndi mitengo ya tende وَحَدَآئِقَ غُلۡبًا ٣٠Ndi minda imene ili ndi mitengo yambiri وَفَٰكِهَةً وَأَبًّا ٣١Ndi mitengo ya zipatso ndi msipu مَّتَٰعًا لَّكُمۡ وَلِأَنۡعَٰمِكُمۡ ٣٢Chakudya cha inu ndi ziweto zanu فَإِذَا جَآءَتِ ٱلصَّآخَّةُ ٣٣Koma pamene kulira kogonthetsa mkhutu kudzamveka يَوۡمَ يَفِرُّ ٱلۡمَرۡءُ مِنۡ أَخِيهِ ٣٤Patsiku limene munthu adzakana m’bale wake وَأُمِّهِۦ وَأَبِيهِ ٣٥Amai ake ndi bambo ake وَصَٰحِبَتِهِۦ وَبَنِيهِ ٣٦Mkazi wake ndi ana ake لِكُلِّ ٱمۡرِيٍٕ مِّنۡهُمۡ يَوۡمَئِذٍ شَأۡنٌ يُغۡنِيهِ ٣٧Chifukwa aliyense patsiku limeneli, adzakhala otangwanika ndi mavuto ake وُجُوهٌ يَوۡمَئِذٍ مُّسۡفِرَةٌ ٣٨Patsiku limeneli padzakhala nkhope zambiri zowala ضَاحِكَةٌ مُّسۡتَبۡشِرَةٌ ٣٩Zosekerera ndi zachimwemwe chifukwa cha nkhani yabwino وَوُجُوهٌ يَوۡمَئِذٍ عَلَيۡهَا غَبَرَةٌ ٤٠Ndipo pa tsikuli padzakhala nkhope zina zokutidwa ndi fumbi تَرۡهَقُهَا قَتَرَةٌ ٤١M’dima udzakuta iwo أُوْلَٰٓئِكَ هُمُ ٱلۡكَفَرَةُ ٱلۡفَجَرَةُ ٤٢Awa adzakhala anthu osakhulupirira ndi ochita zoipa