بِسۡمِ ٱللَّهِ ٱلرَّحۡمَٰنِ ٱلرَّحِيمِ
وَٱلنَّٰزِعَٰتِ غَرۡقًا ١Pali iwo amene amalanda mwankhanza وَٱلنَّٰشِطَٰتِ نَشۡطًا ٢Ndi pali iwo amene amachotsa mwaufulu وَٱلسَّٰبِحَٰتِ سَبۡحًا ٣Ndi pali iwo amene amauluka فَٱلسَّٰبِقَٰتِ سَبۡقًا ٤Ndi pali iwo amene amathamanga ngati ali pa liwiro loopsya فَٱلۡمُدَبِّرَٰتِ أَمۡرًا ٥Ndi pali angelo amene amakwaniritsa kuchita malamulo a Ambuye wawo يَوۡمَ تَرۡجُفُ ٱلرَّاجِفَةُ ٦Patsiku limene dziko ndi mapiri zidzagwedezeka kwambiri تَتۡبَعُهَا ٱلرَّادِفَةُ ٧Ndi kulira kwa lipenga kawiri قُلُوبٌ يَوۡمَئِذٍ وَاجِفَةٌ ٨Mitima, patsiku limeneli, idzafumuka ndi kuda nkhawa أَبۡصَٰرُهَا خَٰشِعَةٌ ٩Maso awo atagwetsa pansi يَقُولُونَ أَءِنَّا لَمَرۡدُودُونَ فِي ٱلۡحَافِرَةِ ١٠Iwo amanena kuti: “Kodi ife tidzabwerera monga momwe tinali poyamba?” أَءِذَا كُنَّا عِظَٰمًا نَّخِرَةً ١١“Angakhale mafupa athu ataola?” قَالُواْ تِلۡكَ إِذًا كَرَّةٌ خَاسِرَةٌ ١٢Iwo amati: “Kubwerera kotero ndi kopanda phindu.” فَإِنَّمَا هِيَ زَجۡرَةٌ وَٰحِدَةٌ ١٣Koma udzakhala mfuwu umodzi okha فَإِذَا هُم بِٱلسَّاهِرَةِ ١٤Pamene, taona, iwo adzadzipeza okha ali pamwamba pa nthaka ali ndi moyo هَلۡ أَتَىٰكَ حَدِيثُ مُوسَىٰٓ ١٥Kodiinumudaimvankhaniya Mose إِذۡ نَادَىٰهُ رَبُّهُۥ بِٱلۡوَادِ ٱلۡمُقَدَّسِ طُوًى ١٦PameneAmbuye wake adamuitana mu dambo lodalitsika la Tuwa ٱذۡهَبۡ إِلَىٰ فِرۡعَوۡنَ إِنَّهُۥ طَغَىٰ ١٧“Pita kwa Farao; Ndithudi iye waphwanya malamulo mopyola muyezo.” فَقُلۡ هَل لَّكَ إِلَىٰٓ أَن تَزَكَّىٰ ١٨“Ndipo ukamuuze kuti: Kodi ungadziyeretse wekha?” وَأَهۡدِيَكَ إِلَىٰ رَبِّكَ فَتَخۡشَىٰ ١٩“Ndi kuti ine ndikulondolere kwa Ambuye wako kuti uzimuopa Iye?” فَأَرَىٰهُ ٱلۡأٓيَةَ ٱلۡكُبۡرَىٰ ٢٠Kotero iye adamuonetsa chizindikiro cha chikulu فَكَذَّبَ وَعَصَىٰ ٢١Koma iye adachikana ndipo sanamvere ثُمَّ أَدۡبَرَ يَسۡعَىٰ ٢٢Iye adapitirizabe kuchita zoipa فَحَشَرَ فَنَادَىٰ ٢٣Ndipo iye adaitana anthu ake onse ndipo anafuula mokweza فَقَالَ أَنَا۠ رَبُّكُمُ ٱلۡأَعۡلَىٰ ٢٤Nati: “Ine ndine Ambuye wanu wapamwamba mwamba.” Al-Naziat فَأَخَذَهُ ٱللَّهُ نَكَالَ ٱلۡأٓخِرَةِ وَٱلۡأُولَىٰٓ ٢٥Motero Mulungu adamugwetsera iye chilango chifukwa cha mau ake omaliza ndi oyamba إِنَّ فِي ذَٰلِكَ لَعِبۡرَةً لِّمَن يَخۡشَىٰٓ ٢٦Ndithudi mu izi muli phunziro lomveka kwa anthu oopa Mulungu ءَأَنتُمۡ أَشَدُّ خَلۡقًا أَمِ ٱلسَّمَآءُۚ بَنَىٰهَا ٢٧Kodi inu ndinu ovuta kulenga kapena thambo la mlengalenga limene Mulungu adalilenga رَفَعَ سَمۡكَهَا فَسَوَّىٰهَا ٢٨Iye analikweza m’mwamba ndi kulikonza bwino وَأَغۡطَشَ لَيۡلَهَا وَأَخۡرَجَ ضُحَىٰهَا ٢٩Usiku wake amaukuta ndi m’dima ndipo masana ake amatulutsa kuwala وَٱلۡأَرۡضَ بَعۡدَ ذَٰلِكَ دَحَىٰهَآ ٣٠Ndipo pambuyo pake adalikulitsa dziko أَخۡرَجَ مِنۡهَا مَآءَهَا وَمَرۡعَىٰهَا ٣١Ndipo anatulutsa madzi ndi msipu وَٱلۡجِبَالَ أَرۡسَىٰهَا ٣٢Ndipo adazika mapiri molimbika مَتَٰعًا لَّكُمۡ وَلِأَنۡعَٰمِكُمۡ ٣٣Chakudya cha phindu kwa inu ndi kwa zoweta zanu فَإِذَا جَآءَتِ ٱلطَّآمَّةُ ٱلۡكُبۡرَىٰ ٣٤Koma pamene mavuto akulu akudza يَوۡمَ يَتَذَكَّرُ ٱلۡإِنسَٰنُ مَا سَعَىٰ ٣٥Tsiku limene munthu adzayamba kuganiza ntchito zake zonse وَبُرِّزَتِ ٱلۡجَحِيمُ لِمَن يَرَىٰ ٣٦Ndipo Gahena idzabweretsedwa pafupi kuti aliyense aione فَأَمَّا مَن طَغَىٰ ٣٧Ndipo kwa iye ophwanya malamulo وَءَاثَرَ ٱلۡحَيَوٰةَ ٱلدُّنۡيَا ٣٨Ndipo anasankha moyo wapadziko lino فَإِنَّ ٱلۡجَحِيمَ هِيَ ٱلۡمَأۡوَىٰ ٣٩Ndithudi malo ake okhala ndi ku Gahena وَأَمَّا مَنۡ خَافَ مَقَامَ رَبِّهِۦ وَنَهَى ٱلنَّفۡسَ عَنِ ٱلۡهَوَىٰ ٤٠Koma kwa iwo amene amaopa kukaima pamaso pa Ambuye wake ndi machimo ndipo anali kudziletsa kuchita chifuniro chopanda pake فَإِنَّ ٱلۡجَنَّةَ هِيَ ٱلۡمَأۡوَىٰ ٤١Ndithudi adzakhala ku Paradiso يَسۡـَٔلُونَكَ عَنِ ٱلسَّاعَةِ أَيَّانَ مُرۡسَىٰهَا ٤٢Amakufunsa za nthawi imene chigumula chidzabwere فِيمَ أَنتَ مِن ذِكۡرَىٰهَآ ٤٣Iwe siudziwa zoti unene china chili chonse إِلَىٰ رَبِّكَ مُنتَهَىٰهَآ ٤٤Ndi Ambuye wako yekha amene amadziwa tsiku إِنَّمَآ أَنتَ مُنذِرُ مَن يَخۡشَىٰهَا ٤٥Iwe ndiwe mchenjezi chabe kwa iwo amene ali kuliopa tsikuli كَأَنَّهُمۡ يَوۡمَ يَرَوۡنَهَا لَمۡ يَلۡبَثُوٓاْ إِلَّا عَشِيَّةً أَوۡ ضُحَىٰهَا ٤٦Patsiku limene iwo adzachiona chigumula, kudzakhala ngati kuti iwo sanakhale padziko lapansi nthawi yaitali koma usiku umodzi kapena usana wokha