Millat al-Islam

Chapter 100 · 11 verses · Al Haji Yusuf Muhammad Kanyamula

Surah Al-Adiyat in Chichewa

Arabic with tafsir Listen to Surah Al-Adiyat (1269 reciters)

بِسۡمِ ٱللَّهِ ٱلرَّحۡمَٰنِ ٱلرَّحِيمِ

وَٱلۡعَٰدِيَٰتِ ضَبۡحًا ١Palizothamangakwambirindikupumakwawokofulumira فَٱلۡمُورِيَٰتِ قَدۡحًا ٢Ndi zimene zimaonetsa moto zikamathamanga فَٱلۡمُغِيرَٰتِ صُبۡحًا ٣Ndipo zimachita nkhondo m’mbandakucha فَأَثَرۡنَ بِهِۦ نَقۡعًا ٤Ndi kuonetsa fumbi فَوَسَطۡنَ بِهِۦ جَمۡعًا ٥Ndi kuphwanya pakati gulu la adani إِنَّ ٱلۡإِنسَٰنَ لِرَبِّهِۦ لَكَنُودٌ ٦Ndithudi! Munthu sathokoza kwaAmbuye wake وَإِنَّهُۥ عَلَىٰ ذَٰلِكَ لَشَهِيدٌ ٧Ndipo mwini wake amachitira umboni zimenezi وَإِنَّهُۥ لِحُبِّ ٱلۡخَيۡرِ لَشَدِيدٌ ٨Ndithudi iye ali kukonda chuma kwambiri ۞ أَفَلَا يَعۡلَمُ إِذَا بُعۡثِرَ مَا فِي ٱلۡقُبُورِ ٩Kodi iye sadziwa kuti pamene zonse zili m’manda zidzatulutsidwa ndi kuonetsedwa poyera وَحُصِّلَ مَا فِي ٱلصُّدُورِ ١٠Ndizonsezimenezilim’mitimayaanthuzizidzaululidwa إِنَّ رَبَّهُم بِهِمۡ يَوۡمَئِذٍ لَّخَبِيرُۢ ١١Ndithudi, patsiku limeneli, Ambuye wako adzakhala ali kudziwa chilichonse

Translation: Al Haji Yusuf Muhammad Kanyamula.