بِسۡمِ ٱللَّهِ ٱلرَّحۡمَٰنِ ٱلرَّحِيمِ
ٱلۡقَارِعَةُ ١Tsiku louka kwa akufa مَا ٱلۡقَارِعَةُ ٢Kodi tsiku louka kwa akufa ndi chiyani وَمَآ أَدۡرَىٰكَ مَا ٱلۡقَارِعَةُ ٣Kodi ndi chiyani chimene chidzakuuze iwe kuti tsiku louka kwa akufa ndi chiani يَوۡمَ يَكُونُ ٱلنَّاسُ كَٱلۡفَرَاشِ ٱلۡمَبۡثُوثِ ٤Ndi tsiku limene anthu adzakhala ngati dzombe louluka paliponse وَتَكُونُ ٱلۡجِبَالُ كَٱلۡعِهۡنِ ٱلۡمَنفُوشِ ٥Ndi mapiri adzakhala ngati fumbefumbe za ubweya فَأَمَّا مَن ثَقُلَتۡ مَوَٰزِينُهُۥ ٦Ndipo iye amene muyeso wake wa ntchito zabwino udzakhala wolemera فَهُوَ فِي عِيشَةٍ رَّاضِيَةٍ ٧Adzakhala ndi moyo wa chimwemwe ndi chisangalalo وَأَمَّا مَنۡ خَفَّتۡ مَوَٰزِينُهُۥ ٨Koma iye amene muyeso wake wa ntchito zabwino udzapezeka wopepuka فَأُمُّهُۥ هَاوِيَةٌ ٩Mudzi wake udzakhala dzenje lamoto وَمَآ أَدۡرَىٰكَ مَا هِيَهۡ ١٠Kodi ndi chiyani chimene chidzakuuze zinthu zonsezi نَارٌ حَامِيَةُۢ ١١Ndi moto wa malawi osatha