السورة بالعربية مع التفسير
استمع إلى سورة الضحى (1,350 قارئاً)
بِسۡمِ ٱللَّهِ ٱلرَّحۡمَٰنِ ٱلرَّحِيمِ
وَٱلضُّحَىٰ ١Pali usana وَٱلَّيۡلِ إِذَا سَجَىٰ ٢Ndi pali usiku pamene ulipo مَا وَدَّعَكَ رَبُّكَ وَمَا قَلَىٰ ٣Ambuye wako sadakutaye iwe ndiponso sakudana nawe ayi وَلَلۡأٓخِرَةُ خَيۡرٌ لَّكَ مِنَ ٱلۡأُولَىٰ ٤Ndipo, ndithudi, moyo umene uli nkudza ndi wabwino kwa iwe kuposa moyo uno وَلَسَوۡفَ يُعۡطِيكَ رَبُّكَ فَتَرۡضَىٰٓ ٥Ndithudi Ambuye wako adzakupatsa, ndipo iwe chidzakukondweretsa أَلَمۡ يَجِدۡكَ يَتِيمًا فَـَٔاوَىٰ ٦Kodi sadakupeze iwe uli wa masiye ndipo adakupatsa malo okhala وَوَجَدَكَ ضَآلًّا فَهَدَىٰ ٧Kodi sadakupeze uli wosochera ndipo Iye adakutsogolera وَوَجَدَكَ عَآئِلًا فَأَغۡنَىٰ ٨Kodi sadakupeze iwe waumphawi ndipo adakulemeretsa فَأَمَّا ٱلۡيَتِيمَ فَلَا تَقۡهَرۡ ٩Motero iwe usapondereze pansi mwana wa masiye وَأَمَّا ٱلسَّآئِلَ فَلَا تَنۡهَرۡ ١٠Ndipo usapirikitse munthu wopempha وَأَمَّا بِنِعۡمَةِ رَبِّكَ فَحَدِّثۡ ١١Koma lengeza chisomo cha a Ambuye wako
الترجمة: Al Haji Yusuf Muhammad Kanyamula.