ملة الإسلام

السورة 92 · 21 آية · Al Haji Yusuf Muhammad Kanyamula

سورة الليل باللغة الشيشيوا

السورة بالعربية مع التفسير استمع إلى سورة الليل (1,297 قارئاً)
مكيةسورة الليل٢١ آية

بِسۡمِ ٱللَّهِ ٱلرَّحۡمَٰنِ ٱلرَّحِيمِ

وَٱلَّيۡلِ إِذَا يَغۡشَىٰ ١Paliusikupamenemdimaumayamba وَٱلنَّهَارِ إِذَا تَجَلَّىٰ ٢Ndimasanapamene kumayera وَمَا خَلَقَ ٱلذَّكَرَ وَٱلۡأُنثَىٰٓ ٣Ndi pali Iye amene adalenga chachimuna ndi chachikazi إِنَّ سَعۡيَكُمۡ لَشَتَّىٰ ٤Ndithudi zochita zanu zonse zili ndi mapeto osiyana فَأَمَّا مَنۡ أَعۡطَىٰ وَٱتَّقَىٰ ٥Akakhala iye amene amapereka chaulere ndipo amamuopa Mulungu وَصَدَّقَ بِٱلۡحُسۡنَىٰ ٦Ndipo amakhulupirira pochita zinthu zabwino فَسَنُيَسِّرُهُۥ لِلۡيُسۡرَىٰ ٧Ife tidzamusalazira njira yake ya ku chipulumutso وَأَمَّا مَنۢ بَخِلَ وَٱسۡتَغۡنَىٰ ٨Koma iye amene sapereka chaulere ndipo amaganiza kuti ndi woima payekha وَكَذَّبَ بِٱلۡحُسۡنَىٰ ٩Sakhulupirira ndipo sachita ntchito zabwino فَسَنُيَسِّرُهُۥ لِلۡعُسۡرَىٰ ١٠Tidzamusalazira njira yake ya ku chionongeko وَمَا يُغۡنِي عَنۡهُ مَالُهُۥٓ إِذَا تَرَدَّىٰٓ ١١Kodi chuma chake chidzamuthandiza chiani pamene iye azidzazunzika إِنَّ عَلَيۡنَا لَلۡهُدَىٰ ١٢Ndithudi ndi udindo wathu kupereka chilangizo وَإِنَّ لَنَا لَلۡأٓخِرَةَ وَٱلۡأُولَىٰ ١٣Ndipo, ndithudi, zonse za m’moyo umene uli nkudza ndi za m’moyo uno ndi zathu فَأَنذَرۡتُكُمۡ نَارًا تَلَظَّىٰ ١٤Motero ndakuchenjezani za moto wa lawilawi لَا يَصۡلَىٰهَآ إِلَّا ٱلۡأَشۡقَى ١٥Kulibe Al-Dhuha 655 munthu amene akapsye nawo kupatula munthu wochita zoipa ٱلَّذِي كَذَّبَ وَتَوَلَّىٰ ١٦Amene amakana choonadi ndipo safuna kumvera chenjezo وَسَيُجَنَّبُهَا ٱلۡأَتۡقَى ١٧Koma anthu onse olungama, adzatalikirana nawo ٱلَّذِي يُؤۡتِي مَالَهُۥ يَتَزَكَّىٰ ١٨Amene amapereka chaulere chake poonjezera kudziyeretsa وَمَا لِأَحَدٍ عِندَهُۥ مِن نِّعۡمَةٍ تُجۡزَىٰٓ ١٩Osati chifukwa chakuti afuna kupezako cholowa ayi إِلَّا ٱبۡتِغَآءَ وَجۡهِ رَبِّهِ ٱلۡأَعۡلَىٰ ٢٠Kupatula ndi cholinga chopeza chisomo cha Ambuye wake, wapamwamba mwamba وَلَسَوۡفَ يَرۡضَىٰ ٢١Ndithudi iye adzasangalala

الترجمة: Al Haji Yusuf Muhammad Kanyamula.