ملة الإسلام

السورة 69 · 52 آية · Al Haji Yusuf Muhammad Kanyamula

سورة الحاقة باللغة الشيشيوا

السورة بالعربية مع التفسير استمع إلى سورة الحاقة (1,346 قارئاً)
مكيةسورة الحاقة٥٢ آية

بِسۡمِ ٱللَّهِ ٱلرَّحۡمَٰنِ ٱلرَّحِيمِ

ٱلۡحَآقَّةُ ١Choonadi chenicheni مَا ٱلۡحَآقَّةُ ٢Kodi choonadi chenicheni ndi chiyani وَمَآ أَدۡرَىٰكَ مَا ٱلۡحَآقَّةُ ٣Kodi ndi chiyani chimene chingakupangitse kuti udziwe kuti choonadi chenicheni ndi chiti كَذَّبَتۡ ثَمُودُ وَعَادُۢ بِٱلۡقَارِعَةِ ٤Mtundu wa Thamoud ndi Ad adakana ola la chionongeko فَأَمَّا ثَمُودُ فَأُهۡلِكُواْ بِٱلطَّاغِيَةِ ٥Ndipo anthu a Thamoud adaonongeka ndi mfuwu woopsya وَأَمَّا عَادٌ فَأُهۡلِكُواْ بِرِيحٍ صَرۡصَرٍ عَاتِيَةٍ ٦Ndipo anthu a Aad adaonongeka ndi chimphepo cha mkuntho سَخَّرَهَا عَلَيۡهِمۡ سَبۡعَ لَيَالٍ وَثَمَٰنِيَةَ أَيَّامٍ حُسُومًاۖ فَتَرَى ٱلۡقَوۡمَ فِيهَا صَرۡعَىٰ كَأَنَّهُمۡ أَعۡجَازُ نَخۡلٍ خَاوِيَةٍ ٧Chimene Mulungu adachilamulira kuti chikunthe pa iwo usiku usanu ndi uwiri ndi usana usanu ndi utatu mosalekeza. Moti iwe ukadawaona anthu atagonagona ukadayesa kuti ndi mitengo ya migwalangwa yakugwa فَهَلۡ تَرَىٰ لَهُم مِّنۢ بَاقِيَةٍ ٨Kodi uli kuona wina wa iwo opulumuka وَجَآءَ فِرۡعَوۡنُ وَمَن قَبۡلَهُۥ وَٱلۡمُؤۡتَفِكَٰتُ بِٱلۡخَاطِئَةِ ٩Ndipo Farao ndi anthu amene adalipo iye asadabadwe, ndi a mizinda imene idaonongeka anali kuchita zoipa فَعَصَوۡاْ رَسُولَ رَبِّهِمۡ فَأَخَذَهُمۡ أَخۡذَةً رَّابِيَةً ١٠Ndipo iwo sanamvere Mtumwi wochokera kwa Ambuye wawo ndipo Iye adawalanga ndi chilango chowawa zedi إِنَّا لَمَّا طَغَا ٱلۡمَآءُ حَمَلۡنَٰكُمۡ فِي ٱلۡجَارِيَةِ ١١Ndithudi!Pamenemadzianasefukira,Ifetidakunyamulani inu m’chombo لِنَجۡعَلَهَا لَكُمۡ تَذۡكِرَةً وَتَعِيَهَآ أُذُنٌ وَٰعِيَةٌ ١٢Kuti tikhoza kuchipanga icho kukhala chikumbutso ndi kuti khutu la kumva limve فَإِذَا نُفِخَ فِي ٱلصُّورِ نَفۡخَةٌ وَٰحِدَةٌ ١٣Ndipo pamene lipenga lidzaimbidwa kamodzi وَحُمِلَتِ ٱلۡأَرۡضُ وَٱلۡجِبَالُ فَدُكَّتَا دَكَّةً وَٰحِدَةً ١٤Ndipo nthaka ndi mapiri anyamulidwa pamodzi ndi kuponyedwa pansi mwamphamvu kamodzi فَيَوۡمَئِذٍ وَقَعَتِ ٱلۡوَاقِعَةُ ١٥Patsiku limeneli chinthu choopsa chidzachitika وَٱنشَقَّتِ ٱلسَّمَآءُ فَهِيَ يَوۡمَئِذٍ وَاهِيَةٌ ١٦Ndipo thambo lidzaphwanyika ndipo lidzakhala lopanda mphamvu وَٱلۡمَلَكُ عَلَىٰٓ أَرۡجَآئِهَاۚ وَيَحۡمِلُ عَرۡشَ رَبِّكَ فَوۡقَهُمۡ يَوۡمَئِذٍ ثَمَٰنِيَةٌ ١٧Ndipo Angelo adzaima mbali zonse ndipo angelo asanu ndi atatu pa tsikuli adzanyamula Mpando wa Chifumu wa Ambuye wako يَوۡمَئِذٍ تُعۡرَضُونَ لَا تَخۡفَىٰ مِنكُمۡ خَافِيَةٌ ١٨Patsiku limeneli mudzaweruzidwa ndipo palibe chinthu chachinsinsi chimene chidzabisika فَأَمَّا مَنۡ أُوتِيَ كِتَٰبَهُۥ بِيَمِينِهِۦ فَيَقُولُ هَآؤُمُ ٱقۡرَءُواْ كِتَٰبِيَهۡ ١٩Ndipo yense amene adzapatsidwa Buku lake kudzanja lamanja adzati: “Ah taonani! Werengani Buku langa!” إِنِّي ظَنَنتُ أَنِّي مُلَٰقٍ حِسَابِيَهۡ ٢٠Ndithudi, ine ndidakhululupira kuti tsiku lina zochita zanga zidzaweruzidwa فَهُوَ فِي عِيشَةٍ رَّاضِيَةٍ ٢١Kotero iye adzakhala ndi moyo wa chisangalalo فِي جَنَّةٍ عَالِيَةٍ ٢٢M’munda wapamwamba قُطُوفُهَا دَانِيَةٌ ٢٣Wa zipatso zokoma zimene zili pafupi كُلُواْ وَٱشۡرَبُواْ هَنِيٓـَٔۢا بِمَآ أَسۡلَفۡتُمۡ فِي ٱلۡأَيَّامِ ٱلۡخَالِيَةِ ٢٤Idyani ndipo imwani mmene mufunire chifukwa cha ntchito zanu zabwino zimene mudatumiza patsogolo panu m’masiku apitawo وَأَمَّا مَنۡ أُوتِيَ كِتَٰبَهُۥ بِشِمَالِهِۦ فَيَقُولُ يَٰلَيۡتَنِي لَمۡ أُوتَ كِتَٰبِيَهۡ ٢٥Koma iye amene adzapatsidwe buku lake m’dzanja lamanzere, adzati: “Kukadakhala bwino ngati Buku langa likadakhala losaperekedwa kwa ine.” وَلَمۡ أَدۡرِ مَا حِسَابِيَهۡ ٢٦“Ndipo sindikadziwa kuti zochita zanga zachuluka bwanji.” يَٰلَيۡتَهَا كَانَتِ ٱلۡقَاضِيَةَ ٢٧“Ikadakhala bwino imfa ikadangodza pa ine.” مَآ أَغۡنَىٰ عَنِّي مَالِيَهۡۜ ٢٨“Chuma changa sichidandithandize chilichonse.” هَلَكَ عَنِّي سُلۡطَٰنِيَهۡ ٢٩“Ulamuliro wanga wonse wachoka kwa ine.” خُذُوهُ فَغُلُّوهُ ٣٠“Mugwireni ndipo mumumange.” ثُمَّ ٱلۡجَحِيمَ صَلُّوهُ ٣١“Ndipo m’ponyeni M’ng’anjo ya moto.” ثُمَّ فِي سِلۡسِلَةٍ ذَرۡعُهَا سَبۡعُونَ ذِرَاعًا فَٱسۡلُكُوهُ ٣٢“Ndipo mumangeni ndi unyolo wotalika malipande makumi asanu ndi awiri.” إِنَّهُۥ كَانَ لَا يُؤۡمِنُ بِٱللَّهِ ٱلۡعَظِيمِ ٣٣Ndithudi, iye samakhulupirira mwa Mulungu wamkulu وَلَا يَحُضُّ عَلَىٰ طَعَامِ ٱلۡمِسۡكِينِ ٣٤Ndipo sadali kuthandiza kudyetsa anthu osowa فَلَيۡسَ لَهُ ٱلۡيَوۡمَ هَٰهُنَا حَمِيمٌ ٣٥Motero lero iye sadzakhala ndi bwenzi aliyense وَلَا طَعَامٌ إِلَّا مِنۡ غِسۡلِينٍ ٣٦Kapena chakudya china chilichonse kupatula zonyasa zochoka pa zilonda لَّا يَأۡكُلُهُۥٓ إِلَّا ٱلۡخَٰطِـُٔونَ ٣٧Palibe amene adzachidya kupatula ochimwa ndi osakhulupilira فَلَآ أُقۡسِمُ بِمَا تُبۡصِرُونَ ٣٨Motero Ine ndilumbira pali chilichonse chimene uli nkuona وَمَا لَا تُبۡصِرُونَ ٣٩Ndi chimene chili chobisika إِنَّهُۥ لَقَوۡلُ رَسُولٍ كَرِيمٍ ٤٠Kuti ndithudi awa ndi mawu a Mtumwi wolemekezeka وَمَا هُوَ بِقَوۡلِ شَاعِرٍۚ قَلِيلًا مَّا تُؤۡمِنُونَ ٤١Ndipo si mawu a Mlakatuli ayi ndipo chikhulupiriro chanu ndi chochepa وَلَا بِقَوۡلِ كَاهِنٍۚ قَلِيلًا مَّا تَذَكَّرُونَ ٤٢Ndipo si mawu a munthu wa maula ayi, ndipo ndi zochepa zimene inu mukumbukira تَنزِيلٌ مِّن رَّبِّ ٱلۡعَٰلَمِينَ ٤٣Ichi ndi chivumbulutso chochokera kwa Ambuye wa zolengedwa zonse وَلَوۡ تَقَوَّلَ عَلَيۡنَا بَعۡضَ ٱلۡأَقَاوِيلِ ٤٤Ndipo iye akanapeka nkhani yokhudza Ife لَأَخَذۡنَا مِنۡهُ بِٱلۡيَمِينِ ٤٥Ndithudi Ife tikadagwira dzanja lake lamanja ثُمَّ لَقَطَعۡنَا مِنۡهُ ٱلۡوَتِينَ ٤٦Ndipo, ndithudi, Ifetikadadulamtsemphawakewamoyo فَمَا مِنكُم مِّنۡ أَحَدٍ عَنۡهُ حَٰجِزِينَ ٤٧Ndipo palibe, wina wa inu, amene akadatiletsa Ife kumugwira وَإِنَّهُۥ لَتَذۡكِرَةٌ لِّلۡمُتَّقِينَ ٤٨Ndipo, ndithudi, Korani iyi ndi chikumbutso kwa iwo amene amapewa zoipa وَإِنَّا لَنَعۡلَمُ أَنَّ مِنكُم مُّكَذِّبِينَ ٤٩Ndipo, ndithudi, Ife timadziwa kuti alipo ena a inu amene amaikana وَإِنَّهُۥ لَحَسۡرَةٌ عَلَى ٱلۡكَٰفِرِينَ ٥٠Ndipo, ndithudi, ilo lidzakhala lomvetsa chisoni kwa anthu osakhulupirira وَإِنَّهُۥ لَحَقُّ ٱلۡيَقِينِ ٥١Ndipo, ndithudi, ichi ndi choonadi chokhachokha فَسَبِّحۡ بِٱسۡمِ رَبِّكَ ٱلۡعَظِيمِ ٥٢Motero lemekeza dzina la Ambuye wako, Wamkulu kulu

الترجمة: Al Haji Yusuf Muhammad Kanyamula.