ملة الإسلام

السورة 68 · 52 آية · Al Haji Yusuf Muhammad Kanyamula

سورة القلم باللغة الشيشيوا

السورة بالعربية مع التفسير استمع إلى سورة القلم (1,276 قارئاً)
مكيةسورة القلم٥٢ آية

بِسۡمِ ٱللَّهِ ٱلرَّحۡمَٰنِ ٱلرَّحِيمِ

نٓۚ وَٱلۡقَلَمِ وَمَا يَسۡطُرُونَ ١Nun. Pali cholembera ndi zimene amalemba مَآ أَنتَ بِنِعۡمَةِ رَبِّكَ بِمَجۡنُونٍ ٢Mwachisomo cha Ambuye wako, sindiwe wamisala ayi وَإِنَّ لَكَ لَأَجۡرًا غَيۡرَ مَمۡنُونٍ ٣Ndithudi iwe udzalandira mphotho yosatha وَإِنَّكَ لَعَلَىٰ خُلُقٍ عَظِيمٍ ٤Ndithudi iwe uli ndi makhalidwe abwino فَسَتُبۡصِرُ وَيُبۡصِرُونَ ٥Iwe udzaona ndipo nawo adzaona بِأَييِّكُمُ ٱلۡمَفۡتُونُ ٦Kuti ndani wa inu amene ndi wamisala إِنَّ رَبَّكَ هُوَ أَعۡلَمُ بِمَن ضَلَّ عَن سَبِيلِهِۦ وَهُوَ أَعۡلَمُ بِٱلۡمُهۡتَدِينَ ٧Ndithudi Ambuye wako amadziwa bwino amene wasochera ku njira yake ndipo amadziwa bwino amene amayenda m’njira yoyenera فَلَا تُطِعِ ٱلۡمُكَذِّبِينَ ٨Motero usatsatire zochita za anthu osakhulupirira وَدُّواْ لَوۡ تُدۡهِنُ فَيُدۡهِنُونَ ٩Iwo afuna utagwirizana nawo kuti nawonso agwirizane nawe وَلَا تُطِعۡ كُلَّ حَلَّافٍ مَّهِينٍ ١٠Ndipo usamvere zonena za munthu wotukwana amene alibe phindu هَمَّازٍ مَّشَّآءِۭ بِنَمِيمٍ ١١Woononga mbiri ya anzake ponena Al Qalam 613 za bodza مَّنَّاعٍ لِّلۡخَيۡرِ مُعۡتَدٍ أَثِيمٍ ١٢Woletsa ntchito zachilungamo, wophwanya malamulo ndi wochita zoipa عُتُلِّۭ بَعۡدَ ذَٰلِكَ زَنِيمٍ ١٣woipa mtima ndipo wobadwa mosalongosoka أَن كَانَ ذَا مَالٍ وَبَنِينَ ١٤Chifukwa iye ali ndi chuma ndi ana إِذَا تُتۡلَىٰ عَلَيۡهِ ءَايَٰتُنَا قَالَ أَسَٰطِيرُ ٱلۡأَوَّلِينَ ١٥Pamene chivumbulutso chathu chilakatulidwa kwa iye, amati: “Ndi nkhani za anthu a makedzana.” سَنَسِمُهُۥ عَلَى ٱلۡخُرۡطُومِ ١٦Ife tidzaika chizindikiro pa mphuno pake إِنَّا بَلَوۡنَٰهُمۡ كَمَا بَلَوۡنَآ أَصۡحَٰبَ ٱلۡجَنَّةِ إِذۡ أَقۡسَمُواْ لَيَصۡرِمُنَّهَا مُصۡبِحِينَ ١٧Ndithudi Ife tidawayesa iwo monga momwe tidawayesera eni ake a munda, amene adalumbira kuti adzakolola mbewu zawo m’mawa mwake وَلَا يَسۡتَثۡنُونَ ١٨Osaonjezera mawu oti: “Ngati Mulungu alola.” فَطَافَ عَلَيۡهَا طَآئِفٌ مِّن رَّبِّكَ وَهُمۡ نَآئِمُونَ ١٩Kotero kudadutsa china chake chochokera kwa Ambuye wako nthawi ya usiku ndi kuwotcha pamene iwo anali kugona فَأَصۡبَحَتۡ كَٱلصَّرِيمِ ٢٠Ndipo m’mawa, munda udasanduka wakuda monga mdima wa usiku فَتَنَادَوۡاْ مُصۡبِحِينَ ٢١Ndipo mmawa iwo adaitanizana wina ndi mnzake أَنِ ٱغۡدُواْ عَلَىٰ حَرۡثِكُمۡ إِن كُنتُمۡ صَٰرِمِينَ ٢٢Nati: “Mulawirire ku munda ngati mufuna kukakolola.” فَٱنطَلَقُواْ وَهُمۡ يَتَخَٰفَتُونَ ٢٣Ndipo iwo adapita, namanong’onezana wina ndi mnzake أَن لَّا يَدۡخُلَنَّهَا ٱلۡيَوۡمَ عَلَيۡكُم مِّسۡكِينٌ ٢٤“Palibe munthu wosauka amene adzaloledwa kulowa m’mundamo kudzapempha” وَغَدَوۡاْ عَلَىٰ حَرۡدٍ قَٰدِرِينَ ٢٥Ndipo m’mawa, onse adapita ndi mphamvu zotchinjirizira anthu osauka فَلَمَّا رَأَوۡهَا قَالُوٓاْ إِنَّا لَضَآلُّونَ ٢٦Koma pamene iwo adaona zimene zidachitika, onse adati: “Ndithudi ife talakwa.” بَلۡ نَحۡنُ مَحۡرُومُونَ ٢٧“Iai! Ndithudi ife tapwetekeka.” قَالَ أَوۡسَطُهُمۡ أَلَمۡ أَقُل لَّكُمۡ لَوۡلَا تُسَبِّحُونَ ٢٨wangwiro amene anali pakati pawo adati: “Kodi ine sindidakuuzeni kuti bwanji inu simunena kuti: Ngati Mulungu alola?” قَالُواْ سُبۡحَٰنَ رَبِّنَآ إِنَّا كُنَّا ظَٰلِمِينَ ٢٩“Iwo adati ulemerero ukhale kwa Ambuye wathu! Ndithudi ife ndife olakwa.” فَأَقۡبَلَ بَعۡضُهُمۡ عَلَىٰ بَعۡضٍ يَتَلَٰوَمُونَ ٣٠Ndipo iwo adayamba kudzudzulana kuti wina adali wolakwa قَالُواْ يَٰوَيۡلَنَآ إِنَّا كُنَّا طَٰغِينَ ٣١Iwo adati: “Tsoka kwa ife! Ndithudi Ife tidali ophwanya malamulo.” عَسَىٰ رَبُّنَآ أَن يُبۡدِلَنَا خَيۡرًا مِّنۡهَآ إِنَّآ إِلَىٰ رَبِّنَا رَٰغِبُونَ ٣٢“Mwina kuti Ambuye wathu adzatipatsa munda wina wabwino m’malo mwa uwu. Ndithudi ndi kwa Iye kumene timapempha modzichepetsa.” كَذَٰلِكَ ٱلۡعَذَابُۖ وَلَعَذَابُ ٱلۡأٓخِرَةِ أَكۡبَرُۚ لَوۡ كَانُواْ يَعۡلَمُونَ ٣٣Chimenechi ndicho chilango koma ndithudi chilango cha m’moyo umene uli nkudza ndi chowawa kwambiri, iwo akadadziwa إِنَّ لِلۡمُتَّقِينَ عِندَ رَبِّهِمۡ جَنَّٰتِ ٱلنَّعِيمِ ٣٤Ndithudi anthu onse angwiro adzalandira minda ya madalitso imene ili ndi Ambuye wawo أَفَنَجۡعَلُ ٱلۡمُسۡلِمِينَ كَٱلۡمُجۡرِمِينَ ٣٥Kodi Ife tidzasamala anthu angwiro chimodzimodzi ndi anthu ochimwa مَا لَكُمۡ كَيۡفَ تَحۡكُمُونَ ٣٦Kodi mwatani? Kodi inu mumaweruza bwanji أَمۡ لَكُمۡ كِتَٰبٌ فِيهِ تَدۡرُسُونَ ٣٧Kapena kodi muli ndi Buku limene mumawerengamo إِنَّ لَكُمۡ فِيهِ لَمَا تَخَيَّرُونَ ٣٨Kuti inu mudzapeza m’menemo chilichonse chimene mukufuna أَمۡ لَكُمۡ أَيۡمَٰنٌ عَلَيۡنَا بَٰلِغَةٌ إِلَىٰ يَوۡمِ ٱلۡقِيَٰمَةِ إِنَّ لَكُمۡ لَمَا تَحۡكُمُونَ ٣٩Kapena inu mwalandira kuchokera kwa Ife, lonjezo lotsimikizika mpaka pa tsiku louka kwa akufa kuti, ndithudi, inu mudzapeza zimene mukufuna سَلۡهُمۡ أَيُّهُم بِذَٰلِكَ زَعِيمٌ ٤٠Tawafunsa ngati wina wa iwo angachitire umboni za lonjezolo أَمۡ لَهُمۡ شُرَكَآءُ فَلۡيَأۡتُواْ بِشُرَكَآئِهِمۡ إِن كَانُواْ صَٰدِقِينَ ٤١Kapena, kodi iwo ali ndi milungu ina? Aleke abweretse milungu yawo ngati iwo anena zoona يَوۡمَ يُكۡشَفُ عَن سَاقٍ وَيُدۡعَوۡنَ إِلَى ٱلسُّجُودِ فَلَا يَسۡتَطِيعُونَ ٤٢Ndipatsikulimenechinthuchoopsachidzachitika, iwo adzaitanidwa kuti apembedze, koma adzalephera kutero خَٰشِعَةً أَبۡصَٰرُهُمۡ تَرۡهَقُهُمۡ ذِلَّةٌۖ وَقَدۡ كَانُواْ يُدۡعَوۡنَ إِلَى ٱلسُّجُودِ وَهُمۡ سَٰلِمُونَ ٤٣Maso awo adzayang’ana pansi ndipo adzanyozedwa kwambiri chifukwa iwo adauzidwa kupembedza pamene adali pa mtendere فَذَرۡنِي وَمَن يُكَذِّبُ بِهَٰذَا ٱلۡحَدِيثِۖ سَنَسۡتَدۡرِجُهُم مِّنۡ حَيۡثُ لَا يَعۡلَمُونَ ٤٤Kotero ndisiyire aliyense amene akutsutsana ndi chenjezo ili. Ife tidzawalanga pang’onopang’ono m’njira imene iwo saizindikira وَأُمۡلِي لَهُمۡۚ إِنَّ كَيۡدِي مَتِينٌ ٤٥Ndipo Ine ndidzalekerera pa kanthawi! Ndithudi chikonzero changa ndi champhamvu أَمۡ تَسۡـَٔلُهُمۡ أَجۡرًا فَهُم مِّن مَّغۡرَمٍ مُّثۡقَلُونَ ٤٦Kapena kodi iwe uli kuwafunsa malipiro moti iwo ali ndi ngongole yambiri أَمۡ عِندَهُمُ ٱلۡغَيۡبُ فَهُمۡ يَكۡتُبُونَ ٤٧Kapena kodi iwo amadziwa za Buku lobisika kuti iwo akhoza kulemba فَٱصۡبِرۡ لِحُكۡمِ رَبِّكَ وَلَا تَكُن كَصَاحِبِ ٱلۡحُوتِ إِذۡ نَادَىٰ وَهُوَ مَكۡظُومٌ ٤٨Motero pirira podikilira chiweruzo cha Ambuye wako ndipo usakhale ngati amene adamezedwa ndi nsomba pamene adalira kupempha chithandizo iye ali m’mavuto لَّوۡلَآ أَن تَدَٰرَكَهُۥ نِعۡمَةٌ مِّن رَّبِّهِۦ لَنُبِذَ بِٱلۡعَرَآءِ وَهُوَ مَذۡمُومٌ ٤٩Ngati Ambuye wake akadapanda kumuonetsa chisomo chake, ndithudi iye akadakhalabe koma iye adaponyedwa pa mtunda pamene anali wolakwa فَٱجۡتَبَٰهُ رَبُّهُۥ فَجَعَلَهُۥ مِنَ ٱلصَّٰلِحِينَ ٥٠Koma Ambuye wake adamusankha ndipo adamuchititsa kukhala wabwino وَإِن يَكَادُ ٱلَّذِينَ كَفَرُواْ لَيُزۡلِقُونَكَ بِأَبۡصَٰرِهِمۡ لَمَّا سَمِعُواْ ٱلذِّكۡرَ وَيَقُولُونَ إِنَّهُۥ لَمَجۡنُونٌ ٥١Ndipo, ndithudi, iwo onse osakhulupirira akadakusokeretsa ndi maso awo pamene amakumbutsidwa ndipo amati: “Ndithudi uyu ndi Wamisala.” وَمَا هُوَ إِلَّا ذِكۡرٌ لِّلۡعَٰلَمِينَ ٥٢Koma ichi si china koma chikumbutso kwa zolengedwa zonse

الترجمة: Al Haji Yusuf Muhammad Kanyamula.