ملة الإسلام

السورة 104 · 9 آية · Al Haji Yusuf Muhammad Kanyamula

سورة الهمزة باللغة الشيشيوا

السورة بالعربية مع التفسير استمع إلى سورة الهمزة (1,287 قارئاً)
مكيةسورة الهمزة٩ آية

بِسۡمِ ٱللَّهِ ٱلرَّحۡمَٰنِ ٱلرَّحِيمِ

وَيۡلٌ لِّكُلِّ هُمَزَةٍ لُّمَزَةٍ ١Tsoka kwa aliyense amene amajeda ndi kuononga mbiri ya anzake ٱلَّذِي جَمَعَ مَالًا وَعَدَّدَهُۥ ٢Amene amasonkhanitsa chuma chake ndi kumachiwerenga يَحۡسَبُ أَنَّ مَالَهُۥٓ أَخۡلَدَهُۥ ٣Iye amaganiza kuti chuma chake chidzamuchititsa iye kukhala ndi moyo wamuyaya كـَلَّاۖ لَيُنۢبَذَنَّ فِي ٱلۡحُطَمَةِ ٤Iyayi! Ndithudi iye adzaponyedwa ku moto woononga وَمَآ أَدۡرَىٰكَ مَا ٱلۡحُطَمَةُ ٥Kodi chidzakuuza kuti moto woononga ndi chiyani نَارُ ٱللَّهِ ٱلۡمُوقَدَةُ ٦Ndi moto wa Mulungu umene Mwini wake anauyatsa ٱلَّتِي تَطَّلِعُ عَلَى ٱلۡأَفۡـِٔدَةِ ٧Umene umafuka m’mitima ya anthu إِنَّهَا عَلَيۡهِم مُّؤۡصَدَةٌ ٨Ndithudi udzawatsekereza mbali iliyonse فِي عَمَدٍ مُّمَدَّدَةِۭ ٩M’sanamila zoima

الترجمة: Al Haji Yusuf Muhammad Kanyamula.