ملة الإسلام

السورة 55 · 78 آية · Al Haji Yusuf Muhammad Kanyamula

سورة الرحمن باللغة الشيشيوا

السورة بالعربية مع التفسير استمع إلى سورة الرحمن (1,425 قارئاً)
مدنيةسورة الرحمن٧٨ آية

بِسۡمِ ٱللَّهِ ٱلرَّحۡمَٰنِ ٱلرَّحِيمِ

ٱلرَّحۡمَٰنُ ١Mwini Chifundo Chosatha عَلَّمَ ٱلۡقُرۡءَانَ ٢Ndiye amene adamphunzitsa munthu Korani خَلَقَ ٱلۡإِنسَٰنَ ٣Ndiye amene adalenga munthu عَلَّمَهُ ٱلۡبَيَانَ ٤Wamuphunzitsa iye mawu anzeru ٱلشَّمۡسُ وَٱلۡقَمَرُ بِحُسۡبَانٍ ٥Dzuwa ndi mwezi zimayenda m’misewu imene zinalamulidwa وَٱلنَّجۡمُ وَٱلشَّجَرُ يَسۡجُدَانِ ٦Zomera (kapena nyenyezi) ndi mitengo zonse zimagwada pomulambira Iye وَٱلسَّمَآءَ رَفَعَهَا وَوَضَعَ ٱلۡمِيزَانَ ٧Iye adakweza kumwamba ndi kukhazikitsa muyeso أَلَّا تَطۡغَوۡاْ فِي ٱلۡمِيزَانِ ٨Kuti inu musaphwanye muyeso وَأَقِيمُواْ ٱلۡوَزۡنَ بِٱلۡقِسۡطِ وَلَا تُخۡسِرُواْ ٱلۡمِيزَانَ ٩Kotero khazikitsani muyeso wachilungamo ndipo musayese monyenga وَٱلۡأَرۡضَ وَضَعَهَا لِلۡأَنَامِ ١٠Ndiye amene adalenga dziko lapansi kuti zolengedwa zake zizikhalamo فِيهَا فَٰكِهَةٌ وَٱلنَّخۡلُ ذَاتُ ٱلۡأَكۡمَامِ ١١Mu ilo muli zipatso ndi mitengo ya tende yobereka phava la zipatso zambiri وَٱلۡحَبُّ ذُو ٱلۡعَصۡفِ وَٱلرَّيۡحَانُ ١٢Ndi chimanga chimene masamba ndi mapesi ake amadyedwa ndi ziweto. Ndi mitengo yonunkhira فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ١٣Kodi ndi zokoma ziti za Ambuye wanu zimene mudzakana خَلَقَ ٱلۡإِنسَٰنَ مِن صَلۡصَٰلٍ كَٱلۡفَخَّارِ ١٤Iye adalenga munthu kuchokera ku dothi monga dothi la mbiya وَخَلَقَ ٱلۡجَآنَّ مِن مَّارِجٍ مِّن نَّارٍ ١٥Ndipo adalenga majini kuchokera kumoto wopanda utsi فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ١٦Kodi ndi zokoma ziti za Ambuye wanu zimene mudzakana رَبُّ ٱلۡمَشۡرِقَيۡنِ وَرَبُّ ٱلۡمَغۡرِبَيۡنِ ١٧Ambuye wa kum’mawa kuwiri ndi Ambuye wa kumadzulo kuwiri فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ١٨Kodi ndi zokoma ziti za Ambuye wanu zimene mudzakana مَرَجَ ٱلۡبَحۡرَيۡنِ يَلۡتَقِيَانِ ١٩Iye adasiya nyanja ziwiri kuti zikumane بَيۡنَهُمَا بَرۡزَخٌ لَّا يَبۡغِيَانِ ٢٠Pakati pawo pali malire amene madzi a uku sangathe kudutsa kupita uko فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ٢١Kodi ndi zokoma ziti za Rahman 573 Ambuye wanu zimene mudzakana يَخۡرُجُ مِنۡهُمَا ٱللُّؤۡلُؤُ وَٱلۡمَرۡجَانُ ٢٢Mu zonse muli nkhombe zazikulu ndi zazing’ono فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ٢٣Kodi ndi zokoma ziti za Ambuye wanu zimene mudzakana وَلَهُ ٱلۡجَوَارِ ٱلۡمُنشَـَٔاتُ فِي ٱلۡبَحۡرِ كَٱلۡأَعۡلَٰمِ ٢٤Ndipo zake ndi zombo zimene zimayenda pa nyanja, zazikulu ngati mapiri فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ٢٥Kodi ndi zokoma ziti za Ambuye wanu zimene mudzakana كُلُّ مَنۡ عَلَيۡهَا فَانٍ ٢٦Zonse zimene zili pa dziko zidzatha وَيَبۡقَىٰ وَجۡهُ رَبِّكَ ذُو ٱلۡجَلَٰلِ وَٱلۡإِكۡرَامِ ٢٧Ndipo nkhope ya Ambuye wako mu Ufumu ndi mu Ulemerero idzakhalabe mpaka kalekale فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ٢٨Kodi ndi zokoma ziti za Ambuye wanu zimene mudzakana يَسۡـَٔلُهُۥ مَن فِي ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِۚ كُلَّ يَوۡمٍ هُوَ فِي شَأۡنٍ ٢٩Zonse zimene zimakhala kumwamba ndi padziko lapansi zimapempha kwa Iye. Tsiku lililonse Iye amakhala ndi chochita فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ٣٠Kodi ndi zokoma ziti za Ambuye wanu zimene mudzakana سَنَفۡرُغُ لَكُمۡ أَيُّهَ ٱلثَّقَلَانِ ٣١Ife tidzadza kwa inu, Oh inu magulu awiri فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ٣٢Kodi ndi zokoma ziti za Ambuye wanu zimene mudzakana يَٰمَعۡشَرَ ٱلۡجِنِّ وَٱلۡإِنسِ إِنِ ٱسۡتَطَعۡتُمۡ أَن تَنفُذُواْ مِنۡ أَقۡطَارِ ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِ فَٱنفُذُواْۚ لَا تَنفُذُونَ إِلَّا بِسُلۡطَٰنٍ ٣٣oh inu gulu la Majini ndi Anthu! Ngati muli ndi mphamvu zodutsa malire a kumwamba ndi dziko lapansi, dutsani. Komatu inu simungadutse popanda chilolezo فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ٣٤Kodi ndi zokoma ziti za Ambuye wanu zimene mudzakana يُرۡسَلُ عَلَيۡكُمَا شُوَاظٌ مِّن نَّارٍ وَنُحَاسٌ فَلَا تَنتَصِرَانِ ٣٥Malawi a moto ndi utsi zidzaponyedwa kwa inu nonse awiri ndipo simudzatha kudziteteza nokha فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ٣٦Kodi ndi zokoma ziti za Ambuye wanu zimene mudzakana فَإِذَا ٱنشَقَّتِ ٱلسَّمَآءُ فَكَانَتۡ وَرۡدَةً كَٱلدِّهَانِ ٣٧Ndi pamene thambo lidzagawanika pakati ndikukhala lofiira ngati mafuta osungunuka فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ٣٨Kodi ndi zokoma ziti za Ambuye wanu zimene mudzakana فَيَوۡمَئِذٍ لَّا يُسۡـَٔلُ عَن ذَنۢبِهِۦٓ إِنسٌ وَلَا جَآنٌّ ٣٩Motero patsiku limeneli, sipadzakhala mafunso kuchokera kwa Munthu kapena Majini okhudza machimo awo فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ٤٠Kodi ndi zokoma ziti za Ambuye wanu zimene mudzakana يُعۡرَفُ ٱلۡمُجۡرِمُونَ بِسِيمَٰهُمۡ فَيُؤۡخَذُ بِٱلنَّوَٰصِي وَٱلۡأَقۡدَامِ ٤١ochimwa adzadziwika ndi zizindikiro ndipo adzawagwira tsumba ndi pamapazi pawo فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ٤٢Kodi ndi zokoma ziti za Ambuye هَٰذِهِۦ جَهَنَّمُ ٱلَّتِي يُكَذِّبُ بِهَا ٱلۡمُجۡرِمُونَ ٤٣Iyi ndi Gahena imene anthu ochimwa amati ndi bodza يَطُوفُونَ بَيۡنَهَا وَبَيۡنَ حَمِيمٍ ءَانٍ ٤٤Iwo adzalowa m’kati mwake ndi m’kati mwa madzi ogaduka فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ٤٥Kodi ndi zokoma ziti za Ambuye wanu zimene mudzakana وَلِمَنۡ خَافَ مَقَامَ رَبِّهِۦ جَنَّتَانِ ٤٦Ndipo kwa iye amene aopa kuima pamaso pa Ambuye wawo, kudzakhala minda iwiri فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ٤٧Kodi ndi zokoma ziti za Ambuye wanu zimene mudzakana ذَوَاتَآ أَفۡنَانٍ ٤٨Zokhala ndi mphanda zotambasuka فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ٤٩Kodi ndi zokoma ziti zaAmbuye wanu zimene mudzakana فِيهِمَا عَيۡنَانِ تَجۡرِيَانِ ٥٠Monse mudzakhala a kasupe awiri otumphuka فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ٥١Kodi ndi zokoma ziti za Ambuye wanu zimene mudzakana فِيهِمَا مِن كُلِّ فَٰكِهَةٍ زَوۡجَانِ ٥٢M’menemu mudzakhala zipatso ziwiriziwiri za mitundumitundu فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ٥٣Kodi ndi zokoma ziti za Ambuye wanu zimene mudzakana مُتَّكِـِٔينَ عَلَىٰ فُرُشِۭ بَطَآئِنُهَا مِنۡ إِسۡتَبۡرَقٍۚ وَجَنَى ٱلۡجَنَّتَيۡنِ دَانٍ ٥٤Iwo adzagona pa makama amene nsalu yake ya m’kati idzakhala yasilika ndipo zipatso za m’minda iwiriyi zidzakhala pafupi pawo فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ٥٥Kodi ndi zokoma ziti za Ambuye wanu zimene mudzakana فِيهِنَّ قَٰصِرَٰتُ ٱلطَّرۡفِ لَمۡ يَطۡمِثۡهُنَّ إِنسٌ قَبۡلَهُمۡ وَلَا جَآنٌّ ٥٦M’menemo mudzakhala wodzisunga ndi ogwetsa nkhope zawo pansi amene Munthu kapena Majini sadawakhudze فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ٥٧Kodi ndi zokoma ziti za Ambuye wanu zimene mudzakana كَأَنَّهُنَّ ٱلۡيَاقُوتُ وَٱلۡمَرۡجَانُ ٥٨olingana ndi miyala ya rubiya ndi ndolo فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ٥٩Kodi ndi zokoma ziti za Ambuye wanu zimene mudzakana هَلۡ جَزَآءُ ٱلۡإِحۡسَٰنِ إِلَّا ٱلۡإِحۡسَٰنُ ٦٠Kodi dipo la ntchito yabwino lingakhale lina loposa ubwino فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ٦١Kodi ndi zokoma ziti za Ambuye wanu zimene mudzakana وَمِن دُونِهِمَا جَنَّتَانِ ٦٢Ndipo poonjezera pa minda iwiri pali minda ina iwiri فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ٦٣Kodi ndi zokoma ziti za Ambuye wanu zimene mudzakana مُدۡهَآمَّتَانِ ٦٤Yooneka mobiriwira فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ٦٥Kodi ndi zokoma ziti za Ambuye wanu zimene mudzakana فِيهِمَا عَيۡنَانِ نَضَّاخَتَانِ ٦٦Monse mudzakhala a kasupe awiri otulutsa madzi ochuluka فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ٦٧Kodi ndi zokoma ziti za Ambuye wanu zimene mudzakana فِيهِمَا فَٰكِهَةٌ وَنَخۡلٌ وَرُمَّانٌ ٦٨Monse mudzakhala zipatso, tende ndi chimanga chachizungu فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ٦٩Kodi ndi zokoma ziti za Ambuye wanu zimene mudzakana فِيهِنَّ خَيۡرَٰتٌ حِسَانٌ ٧٠Mmenemo mudzakhala zinthu zokongola فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ٧١Kodi ndi zokoma ziti za Ambuye wanu zimene mudzakana حُورٌ مَّقۡصُورَٰتٌ فِي ٱلۡخِيَامِ ٧٢Angwiro ndi okhala m’mahema فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ٧٣Kodi ndi zokoma ziti za Ambuye wanu zimene mudzakana لَمۡ يَطۡمِثۡهُنَّ إِنسٌ قَبۡلَهُمۡ وَلَا جَآنٌّ ٧٤Amene Munthu kapena Majini sadawakhudze فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ٧٥Kodi ndi zokoma ziti za Ambuye wanu zimene mudzakana مُتَّكِـِٔينَ عَلَىٰ رَفۡرَفٍ خُضۡرٍ وَعَبۡقَرِيٍّ حِسَانٍ ٧٦Atakhala pa mipando yawofowofo, yobiriwira ndi mabedi okongola فَبِأَيِّ ءَالَآءِ رَبِّكُمَا تُكَذِّبَانِ ٧٧Kodi ndi zokoma ziti za Ambuye wanu zimene mudzakana تَبَٰرَكَ ٱسۡمُ رَبِّكَ ذِي ٱلۡجَلَٰلِ وَٱلۡإِكۡرَامِ ٧٨Lidalitsike dzina la Ambuye wako, Mwini ulemerero, chuma ndi ulemu

الترجمة: Al Haji Yusuf Muhammad Kanyamula.