بِسۡمِ ٱللَّهِ ٱلرَّحۡمَٰنِ ٱلرَّحِيمِ
إِذَا ٱلشَّمۡسُ كُوِّرَتۡ ١Pamene dzuwa lidzavundikiridwa وَإِذَا ٱلنُّجُومُ ٱنكَدَرَتۡ ٢Ndi pamene nyenyezi zidzagwa pansi وَإِذَا ٱلۡجِبَالُ سُيِّرَتۡ ٣Ndi pamene mapiri adzachotsedwa وَإِذَا ٱلۡعِشَارُ عُطِّلَتۡ ٤Ndi pamene ngamila zabele zizakhala zosasamalidwa وَإِذَا ٱلۡوُحُوشُ حُشِرَتۡ ٥Ndi nyama za m’tchire zidzasonkhanitsidwa pamodzi وَإِذَا ٱلۡبِحَارُ سُجِّرَتۡ ٦Ndi pamene nyanja zidzayatsidwa moto kapena zidzasefukira وَإِذَا ٱلنُّفُوسُ زُوِّجَتۡ ٧Ndi pamene mizimu idzakumanitsidwa ndi matupi awo وَإِذَا ٱلۡمَوۡءُۥدَةُ سُئِلَتۡ ٨Ndi pamene mwana wa mkazi wa mng’ono, amene adaundilidwa wa moyo adzafunsidwa بِأَيِّ ذَنۢبٍ قُتِلَتۡ ٩Chifukwa chimene anamuphera وَإِذَا ٱلصُّحُفُ نُشِرَتۡ ١٠Ndi pamene mabuku olembamo ntchito za munthu aliyense adzatulutsidwa وَإِذَا ٱلسَّمَآءُ كُشِطَتۡ ١١Ndi pamene kumwamba kudzafafanizidwa ndi kuchotsedwa ku malo ake وَإِذَا ٱلۡجَحِيمُ سُعِّرَتۡ ١٢Ndi pamene Gahena idzatenthetsedwa kwambiri وَإِذَا ٱلۡجَنَّةُ أُزۡلِفَتۡ ١٣Ndi pamene Paradiso idzafikitsidwa pafupi عَلِمَتۡ نَفۡسٌ مَّآ أَحۡضَرَتۡ ١٤Ndithudi munthu aliyense adzadziwa chimene adachita فَلَآ أُقۡسِمُ بِٱلۡخُنَّسِ ١٥Motero, ndithudi, Ine ndili kulumbira pali nyenyezi zimene zimalowa ٱلۡجَوَارِ ٱلۡكُنَّسِ ١٦Ndi pali maiko zimene zimayenda mofulumira ndi kudzibisa okha وَٱلَّيۡلِ إِذَا عَسۡعَسَ ١٧Ndi pali usiku pamene uchoka وَٱلصُّبۡحِ إِذَا تَنَفَّسَ ١٨Ndipalim’mawapamenekulikucha إِنَّهُۥ لَقَوۡلُ رَسُولٍ كَرِيمٍ ١٩Ndithudi awa ndi Mau a Mtumwi wolemekezeka ذِي قُوَّةٍ عِندَ ذِي ٱلۡعَرۡشِ مَكِينٍ ٢٠Mwini mphamvu amene amalemekezedwa ndi Ambuye, Mwini Mpando wa Chifumu مُّطَاعٍ ثَمَّ أَمِينٍ ٢١Amamveredwa ndi wokhulupirika وَمَا صَاحِبُكُم بِمَجۡنُونٍ ٢٢Ndipo m’bale wanu uyu si wa misala ayi وَلَقَدۡ رَءَاهُ بِٱلۡأُفُقِ ٱلۡمُبِينِ ٢٣Ndipo, ndithudi, iye adamuona iye mu mlengalenga وَمَا هُوَ عَلَى ٱلۡغَيۡبِ بِضَنِينٍ ٢٤Iye sabisa zinthu zosaoneka وَمَا هُوَ بِقَوۡلِ شَيۡطَٰنٍ رَّجِيمٍ ٢٥Ndipo zimene alankhula sizochokera kwa Satana wotembereredwa فَأَيۡنَ تَذۡهَبُونَ ٢٦Kodi inu muli kupita kuti إِنۡ هُوَ إِلَّا ذِكۡرٌ لِّلۡعَٰلَمِينَ ٢٧Ndithudi ichi si china chilichonse ayi koma chikumbutso kwa anthu a mitundu yonse لِمَن شَآءَ مِنكُمۡ أَن يَسۡتَقِيمَ ٢٨Kwa aliyense wa inu amene afuna kuyenda moongoka وَمَا تَشَآءُونَ إِلَّآ أَن يَشَآءَ ٱللَّهُ رَبُّ ٱلۡعَٰلَمِينَ ٢٩Koma inu simungathe kutero pokhapokha ndi chifuniro cha Mulungu, Ambuye wa zolengedwe zonse