لِإِيلَٰفِ قُرَيۡشٍ ١Pofuna kuteteza mtundu wa Quraishإِۦلَٰفِهِمۡ رِحۡلَةَ ٱلشِّتَآءِ وَٱلصَّيۡفِ ٢Kuti apitirire pa maulendo nthawi ya Chilimwe ndi m’nthawi ya Chisanuفَلۡيَعۡبُدُواْ رَبَّ هَٰذَا ٱلۡبَيۡتِ ٣Motero auzeni kuti azipembedza Ambuye wa Nyumba inoٱلَّذِيٓ أَطۡعَمَهُم مِّن جُوعٍ وَءَامَنَهُم مِّنۡ خَوۡفِۭ٤Amene wawadyetsa m’masiku a njala ndi kuwachotsa mantha