السورة بالعربية مع التفسير
استمع إلى سورة الماعون (839 قارئاً)
بِسۡمِ ٱللَّهِ ٱلرَّحۡمَٰنِ ٱلرَّحِيمِ
أَرَءَيۡتَ ٱلَّذِي يُكَذِّبُ بِٱلدِّينِ ١Kodi wamuona munthu amene amakana kuti kuli tsiku la chiweruzo فَذَٰلِكَ ٱلَّذِي يَدُعُّ ٱلۡيَتِيمَ ٢Iye ndiye amene amazunza mwana wamasiye وَلَا يَحُضُّ عَلَىٰ طَعَامِ ٱلۡمِسۡكِينِ ٣Ndipo sakakamiza anthu ena kuti azidyetsa anthu osauka فَوَيۡلٌ لِّلۡمُصَلِّينَ ٤Motero tsoka kwa iwo amene amapemphera ٱلَّذِينَ هُمۡ عَن صَلَاتِهِمۡ سَاهُونَ ٥Amene salabadira mapemphero awo ٱلَّذِينَ هُمۡ يُرَآءُونَ ٦Amene amachita zabwino pofuna kuti ena awaone وَيَمۡنَعُونَ ٱلۡمَاعُونَ ٧Ndipo amakana kupereka chaulere
الترجمة: Al Haji Yusuf Muhammad Kanyamula.