ملة الإسلام

السورة 112 · 4 آية · Khaled Ibrahim Betala

سورة الإخلاص باللغة الشيشيوا

السورة بالعربية مع التفسير استمع إلى سورة الإخلاص (1,405 قارئاً)
مكيةسورة الإخلاص٤ آية

بِسۡمِ ٱللَّهِ ٱلرَّحۡمَٰنِ ٱلرَّحِيمِ

قُلۡ هُوَ ٱللَّهُ أَحَدٌ ١“Nena (iwe Mtumiki (s.a.w), kwa amene akukufunsa mwachipongwe, mbiri za Mulungu wako): “Iye ndi Allah Mmodzi, (alibe mnzake) ٱللَّهُ ٱلصَّمَدُ ٢“Allah ndi Wokhala ndi zonse Wodaliridwa ndi zolengedwa Zake لَمۡ يَلِدۡ وَلَمۡ يُولَدۡ ٣“Sadabale (mwana) ndiponso sadaberekedwe وَلَمۡ يَكُن لَّهُۥ كُفُوًا أَحَدُۢ ٤“Ndiponso palibe aliyense wofanana ndi Iye.”

الترجمة: Khaled Ibrahim Betala.