ملة الإسلام

السورة 111 · 5 آية · Khaled Ibrahim Betala

سورة المسد باللغة الشيشيوا

السورة بالعربية مع التفسير استمع إلى سورة المسد (1,267 قارئاً)
مكيةسورة المسد٥ آية

بِسۡمِ ٱللَّهِ ٱلرَّحۡمَٰنِ ٱلرَّحِيمِ

تَبَّتۡ يَدَآ أَبِي لَهَبٍ وَتَبَّ ١“Aonongeka manja a Abi Lahab (omwe adali kuwagwiritsa ntchito pozunza Asilamu). Nayenso wawonongeka مَآ أَغۡنَىٰ عَنۡهُ مَالُهُۥ وَمَا كَسَبَ ٢“Chuma chake ndi ulemelero wake (umene adaupeza) sizidamthandize ku chilango cha Allah سَيَصۡلَىٰ نَارًا ذَاتَ لَهَبٍ ٣“Adzalowa ku Moto wa malawi وَٱمۡرَأَتُهُۥ حَمَّالَةَ ٱلۡحَطَبِ ٤“Nayenso mkazi wake (adzalowa ku Moto) yemwe adali kusenza nkhuni (za minga pomutchera Mtumiki (s.a.w) komanso amanka nadanitsa pakati pa anthu فِي جِيدِهَا حَبۡلٌ مِّن مَّسَدِۭ ٥“Mkhosi mwake mdzamangidwa chingwe chopiringidwa bwino cha mlaza (chomlanga nacho)

الترجمة: Khaled Ibrahim Betala.