ملة الإسلام

السورة 107 · 7 آية · Khaled Ibrahim Betala

سورة الماعون باللغة الشيشيوا

السورة بالعربية مع التفسير استمع إلى سورة الماعون (839 قارئاً)
مكيةسورة الماعون٧ آية

بِسۡمِ ٱللَّهِ ٱلرَّحۡمَٰنِ ٱلرَّحِيمِ

أَرَءَيۡتَ ٱلَّذِي يُكَذِّبُ بِٱلدِّينِ ١“Kodi wamuona yemwe akutsutsa za mphoto (ndi chiwerengero cha tsiku lachimaliziro) فَذَٰلِكَ ٱلَّذِي يَدُعُّ ٱلۡيَتِيمَ ٢“Iye ndi yemwe akukankha wamasiye (mwankhanza) وَلَا يَحُضُّ عَلَىٰ طَعَامِ ٱلۡمِسۡكِينِ ٣“Ndipo salimbikitsa (ena pamodzi ndi iye mwini) kudyetsa osauka فَوَيۡلٌ لِّلۡمُصَلِّينَ ٤“Choncho kuonongeka kuli pa ena mwa opemphera swala (amene ali ndi mbiri izi) ٱلَّذِينَ هُمۡ عَن صَلَاتِهِمۡ سَاهُونَ ٥“Omwe amachitira mphwayi mapemphero awo ٱلَّذِينَ هُمۡ يُرَآءُونَ ٦“Amenenso (akamachita mapemphero awo) amadzionetsera (kwa anthu mwachipha maso kuti apeze ulemelero ndi kutamandidwa mmitima mwa anthu) وَيَمۡنَعُونَ ٱلۡمَاعُونَ ٧“Ndipo amamana ziwiya (zawo posabwereka anzawo zinthu zofunika pa moyo wa aliyense monga nkhwangwa, mpeni, mtondo ndi zina zotere)

الترجمة: Khaled Ibrahim Betala.