بِسۡمِ ٱللَّهِ ٱلرَّحۡمَٰنِ ٱلرَّحِيمِ
يَٰٓأَيُّهَا ٱلۡمُدَّثِّرُ ١ohiweamenewakutidwa قُمۡ فَأَنذِرۡ ٢Dzukandikuperekachenjezo وَرَبَّكَ فَكَبِّرۡ ٣Ndipo lemekeza Ambuye wako وَثِيَابَكَ فَطَهِّرۡ ٤Ndipo yeretsa zovala zako وَٱلرُّجۡزَ فَٱهۡجُرۡ ٥Ndipo pewa zonse za mafano وَلَا تَمۡنُن تَسۡتَكۡثِرُ ٦Ndipo usapereke thandizo ndi cholinga chopezamo cholowa وَلِرَبِّكَ فَٱصۡبِرۡ ٧Ndipo khala wopirira chifukwa cha Ambuye wako فَإِذَا نُقِرَ فِي ٱلنَّاقُورِ ٨Ndipo pamene lipenga lidzalira فَذَٰلِكَ يَوۡمَئِذٍ يَوۡمٌ عَسِيرٌ ٩Ndithudi limeneli lidzakhala tsiku loopsa عَلَى ٱلۡكَٰفِرِينَ غَيۡرُ يَسِيرٍ ١٠Tsiku lamavuto kwa anthu onse osakhulupirira ذَرۡنِي وَمَنۡ خَلَقۡتُ وَحِيدًا ١١Ndisiye ndekha kuthana ndi munthu amene ndidamulenga ndekha وَجَعَلۡتُ لَهُۥ مَالًا مَّمۡدُودًا ١٢Ndipo ndidamupatsa chuma chosawerengeka وَبَنِينَ شُهُودًا ١٣Ndi ana okhala pambali pake وَمَهَّدتُّ لَهُۥ تَمۡهِيدًا ١٤Ndipo Ine ndidamuchitira zonse kuti zikhale zolongosoka ndi zapafupi ثُمَّ يَطۡمَعُ أَنۡ أَزِيدَ ١٥Koma nthawi zonse amafuna kuti ndizimupatsabe zinthu zambiri كـَلَّآۖ إِنَّهُۥ كَانَ لِأٓيَٰتِنَا عَنِيدًا ١٦Kosatheka! Ndithudi iye wakhala ali kuchitira mwano chivumbulutso chathu سَأُرۡهِقُهُۥ صَعُودًا ١٧Ine ndidzamukhaulitsa pomupatsa chilango chowawa إِنَّهُۥ فَكَّرَ وَقَدَّرَ ١٨Ndithudi iye adaganiza ndipo adakonza chiwembu فَقُتِلَ كَيۡفَ قَدَّرَ ١٩Ndipo ayenera kutembererewa chifukwa cha chiwembu chake ثُمَّ قُتِلَ كَيۡفَ قَدَّرَ ٢٠Motero iye ayenera kutembereredwa chifukwa cha chiwembu chake ثُمَّ نَظَرَ ٢١Ndipo iye anayang’ana ثُمَّ عَبَسَ وَبَسَرَ ٢٢Ndipo iye adachita matsinya ndipo anaonetsa kuipidwa ثُمَّ أَدۡبَرَ وَٱسۡتَكۡبَرَ ٢٣Kenaka adatembenukira kumbali modzikweza فَقَالَ إِنۡ هَٰذَآ إِلَّا سِحۡرٌ يُؤۡثَرُ ٢٤Ndipo iye adati: “Ichi sichina koma matsenga a anthu a amakedzana!” إِنۡ هَٰذَآ إِلَّا قَوۡلُ ٱلۡبَشَرِ ٢٥“Ichi sichina koma mawu a munthu chabe.” سَأُصۡلِيهِ سَقَرَ ٢٦Ine ndidzamuponya iye ku Gahena وَمَآ أَدۡرَىٰكَ مَا سَقَرُ ٢٧Kodi chidzakudziwitsa kuti moto wa ku Gahena ndi chiani لَا تُبۡقِي وَلَا تَذَرُ ٢٨Iwo susunga kapena kusiya لَوَّاحَةٌ لِّلۡبَشَرِ ٢٩Umatentha matupi عَلَيۡهَا تِسۡعَةَ عَشَرَ ٣٠Umasamalidwandiangelokhumindiasanundianayi وَمَا جَعَلۡنَآ أَصۡحَٰبَ ٱلنَّارِ إِلَّا مَلَٰٓئِكَةًۖ وَمَا جَعَلۡنَا عِدَّتَهُمۡ إِلَّا فِتۡنَةً لِّلَّذِينَ كَفَرُواْ لِيَسۡتَيۡقِنَ ٱلَّذِينَ أُوتُواْ ٱلۡكِتَٰبَ وَيَزۡدَادَ ٱلَّذِينَ ءَامَنُوٓاْ إِيمَٰنًا وَلَا يَرۡتَابَ ٱلَّذِينَ أُوتُواْ ٱلۡكِتَٰبَ وَٱلۡمُؤۡمِنُونَ وَلِيَقُولَ ٱلَّذِينَ فِي قُلُوبِهِم مَّرَضٌ وَٱلۡكَٰفِرُونَ مَاذَآ أَرَادَ ٱللَّهُ بِهَٰذَا مَثَلًاۚ كَذَٰلِكَ يُضِلُّ ٱللَّهُ مَن يَشَآءُ وَيَهۡدِي مَن يَشَآءُۚ وَمَا يَعۡلَمُ جُنُودَ رَبِّكَ إِلَّا هُوَۚ وَمَا هِيَ إِلَّا ذِكۡرَىٰ لِلۡبَشَرِ ٣١Ife sitidasankhe wina aliyense koma angelo kuti aziyang’anira moto ndipo tinakhazikitsa chiwerengero chawo ngati mayesero kwa anthu osakhulupirira, kuti iwo onse amene alandira mawu a Mulungu akhulupirire ndi kuti anthu okhulupirira m’choonadi apitirize chikhulupiriro chawo; kuti iwo amene adalandira kale mawu a Mulungu ndiponso anthu onse okhulupirira moona asakhale ndi chikaiko china chilichonse; ndipo kuti onse amene m’mitima mwawo muli matenda pamodzi ndi anthu osakhulupirira anganene kuti: “Kodi Mulungu afuna kutanthauza chiyani pa chitsanzo chotere?” Mmenemo ndi mmene Mulungu amasokeretsera munthu aliyense amene Iye wamufuna ndi kutsogolera aliyense amene Iye wamufuna. Palibe munthu amene amadziwa asirikali a Ambuye wako kupatula Iye mwini. Ichi si china chilichonse koma chikumbutso kwa anthu onse كـَلَّا وَٱلۡقَمَرِ ٣٢Iyayi, ndilumbira pali mwezi وَٱلَّيۡلِ إِذۡ أَدۡبَرَ ٣٣Ndi pali usiku pamene uli n’kutha وَٱلصُّبۡحِ إِذَآ أَسۡفَرَ ٣٤Ndi pali m’mbandakucha pamene uli n’kudza إِنَّهَا لَإِحۡدَى ٱلۡكُبَرِ ٣٥Ndithudi ili ndi limodzi la masoka akuluakulu نَذِيرًا لِّلۡبَشَرِ ٣٦Ndi chenjezo kwa anthu onse لِمَن شَآءَ مِنكُمۡ أَن يَتَقَدَّمَ أَوۡ يَتَأَخَّرَ ٣٧Kwa yense wa inu amene afuna kupitirirabe mtsogolo kapena afuna kutsalira m’mbuyo كُلُّ نَفۡسِۭ بِمَا كَسَبَتۡ رَهِينَةٌ ٣٨Munthu aliyense adzafunsidwa molingana ndi ntchito zake إِلَّآ أَصۡحَٰبَ ٱلۡيَمِينِ ٣٩Kupatula iwo amene adzakhala kudzanja lamanja فِي جَنَّٰتٍ يَتَسَآءَلُونَ ٤٠M’minda, iwo azidzafunsana wina ndi mnzake. Qiyamah عَنِ ٱلۡمُجۡرِمِينَ ٤١Za anthu ochimwa kuti مَا سَلَكَكُمۡ فِي سَقَرَ ٤٢Kodi ndi chiyani chimene chakulowetsani inu ku moto قَالُواْ لَمۡ نَكُ مِنَ ٱلۡمُصَلِّينَ ٤٣Iwo adzayankha nati: “Ife sitimapemphera.” وَلَمۡ نَكُ نُطۡعِمُ ٱلۡمِسۡكِينَ ٤٤Ndiponso sitimadyetsa anthu a njala وَكُنَّا نَخُوضُ مَعَ ٱلۡخَآئِضِينَ ٤٥Ife timangotsutsa zinthu mwaumbuli وَكُنَّا نُكَذِّبُ بِيَوۡمِ ٱلدِّينِ ٤٦Ndipo tidali kunena kuti kulibe tsiku lachiweruzo حَتَّىٰٓ أَتَىٰنَا ٱلۡيَقِينُ ٤٧Mpaka pamene imfa idatipeza فَمَا تَنفَعُهُمۡ شَفَٰعَةُ ٱلشَّٰفِعِينَ ٤٨Motero palibe chidandaulo chochokera kwa wina aliyense chimene chidzamveka فَمَا لَهُمۡ عَنِ ٱلتَّذۡكِرَةِ مُعۡرِضِينَ ٤٩Kodindichifukwachiyaniiwoalikuthawachikumbutso ichi كَأَنَّهُمۡ حُمُرٌ مُّسۡتَنفِرَةٌ ٥٠Monga abulu odzidzimutsidwa فَرَّتۡ مِن قَسۡوَرَةِۭ ٥١omwe anali kuthawa Mlenje, Mkango kapena nyama ina yoopsya بَلۡ يُرِيدُ كُلُّ ٱمۡرِيٍٕ مِّنۡهُمۡ أَن يُؤۡتَىٰ صُحُفًا مُّنَشَّرَةً ٥٢Iai! Aliyense wa iwo afuna kuti apatsidwe masamba a Buku otambasula كـَلَّاۖ بَل لَّا يَخَافُونَ ٱلۡأٓخِرَةَ ٥٣Ndikosatheka! Koma iwo alibe mantha ndi zimene zili nkudza كـَلَّآ إِنَّهُۥ تَذۡكِرَةٌ ٥٤Iyayi. Ndithudi ili ndi chenjezo فَمَن شَآءَ ذَكَرَهُۥ ٥٥Motero musiyeni amene afuna kuti awerenge ndi kulandira chenjezo وَمَا يَذۡكُرُونَ إِلَّآ أَن يَشَآءَ ٱللَّهُۚ هُوَ أَهۡلُ ٱلتَّقۡوَىٰ وَأَهۡلُ ٱلۡمَغۡفِرَةِ ٥٦Ndipo iwo sadzalandira chenjezo pokha pokha ngati Mulungu afuna. Iye ndiye Ambuye wofunika kuti anthu onse azichita mantha ndi Iye, ndipo Iye ndi Ambuye wokhululukira